Soundtracks: A B C D E F G H I J K L M N O P Q R S T U V W X Y Z #

List of artists: A B C D E F G H I J K L M N O P Q R S T U V W X Y Z #


Mthunzi Lyrics


Artist: Langwan Piksy

 

Mthunzi Lyrics

Mthunzi by Langwan Piksy


CHORUS
Ndikufuna mthunziwo
Sindufuna Nkhunizo
Chonde musadule
Mtengo wangawo
Nthawi zina sitikamba zofunika kukambidwa
Sitikankha zofunika kukankhidwa
Pena Sitikanda pofunika kukandidwa
Dziko linasintha timaopa kutayidwa
Ma born again
Sangacheze nawe unless you born again
But then again
Ndingasinthe bwanji ngati muku leader life ngati muli kumwamba kale
U seem so far away
Yesu anadzera ochimwa
Miyala yokanidwayo
These days ndiimene ikusalidwayo
Think again
If you really born again
Njira yanuyo tilondolereni
CHORUS
Ndikufuna mthunziwo
Sindufuna Nkhunizo
Chonde musadule
Mtengo wangawo
Abambo prophet akazi awo prophetess
Chondidabwitsa amakhala ndi confidence
Ine I thought zimayendera maitanidwe
Mesa ndimphatso
Yoti ena alibe
Pa banja panu mwayambisa yanu church
Dzina lake pa Google mwachita search
Tilibe mphavu zokupangirani judge
Koma ngati nku jahena chonde msatipange drag
Kuuza anthu amu mpingo mwanu alemera
Akhristu anu kupusa amayamba kusekelera
Amen!
Mulungu achita kothekera
Kusiya kulimbikira ntchito nkumangopemphera
Kenako amayamba nsanje
Mwawasocheretsa
Kukhulupira ulosi wanu mwawasokoneza
Awa nga satanic
Awa kukhwima chabe awa
Neba wachikunja walemera mtima ukuwawa
CHORUS
Ndikufuna mthunziwo
Sindufuna Nkhunizo
Chonde musadule
Mtengo wangawo
Mutiuze za kumwamba
Osati kumangotikomedwetsa nzapadziko pano
Pano
Muzinthu zonse, zonse zonse
Ambuye akhalemo
Amatero malembo
Upindulanji ndi za mdziko ukutaya moyo wako?
Musachulutse zokamba kuti tidzikuopani
Tidzikweza Mulungu osati tidzikupopani
Tidziona umulungu tikamakuonani
Sing along to the song
Muzinthu zonse, zonse, zonse
Muzinthu zonse Ambuye akhalemo
CHORUS
Ndikufuna mthunziwo
Sindufuna Nkhunizo
Chonde musadule
Mtengo wangawo



A-Z Lyrics Universe

Lyrics / song texts are property and copyright of their owners and provided for educational purposes.